Psalms 74:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudatswanya mitu ya Leviyatani, chilombo cham'madzi chija, nkuitaya kuti ikhale chakudya cha zilombo zam'chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudaphwanya mitu ya Leviyatani; mudampereka akhale chakudya cha zilombo za m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinu amene munaphwanya mitu ya Leviyatani ndi kuyipereka ngati chakudya cha zirombo za mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudaphwanya mitu ya livyatanu; Mudampereka akhale cakudya ca iwo a m'cipululu.