Psalms 74:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudalenga usana ndi usiku. Mudaika mwezi ndi dzuŵa m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masana ndi anu ndipo usiku ndi wanunso; Inuyo munakhazikitsa dzuwa ndi mwezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu: Munakonza kuunika ndi dzuwa.