Psalms 74:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musati mupereke moyo wa nkhunda yanu Israele ku zilombo zakuthengo. Musaiŵale mpaka muyaya moyo wa anthu anu osauka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musapereke moyo wa njiwa yanu kwa chilombo; musamaiwala moyo wa ozunzika anu nthawi yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musapereke moyo wa nkhunda yanu ku zirombo zakuthengo; nthawi zonse musayiwale miyoyo ya anthu anu osautsidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musapereke moyo wa njiwa yanu kwa cirombo; Musamaiwala moyo wa ozunzika anu nthawi yonse.