Psalms 74:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalole kuti anthu oponderezedwa achite manyazi. Osauka ndi osoŵa akutamandeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Okhalira mphanthi asabwere nao manyazi; wozunzika ndi waumphawi alemekeze dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musalole kuti osautsidwa abwerere mwamanyazi; osauka ndi osowa atamande dzina lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Okhalira mphanthi asabwere nao manyazi; Wozunzika ndi waumphawi alemekeze dzina lanu.