Psalms 74:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzayendereni mabwinja oonongeka kwathunthuŵa. Adani aononga zinthu zonse za m'Nyumba yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyamulani mapazi anu kukapenya mapasukidwe osatha, zoipa zonse adazichita mdani m'malo opatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tembenuzani mapazi kuloza ku mabwinja awa amuyaya chiwonongeko ichi chonse mdani wabweretsa pa malo opatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyamulani mapazi anu kukapenya mapasukidwe osatha, Zoipa zonse adazicita mdani m'malo opatulika.