Psalms 74:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani anu abangula m'malo anu opatulika, adaikamo mbendera zao kusonyeza kuti agonjetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Otsutsana ndi Inu abangula pakati pa msonkhano wanu; aika mbendera zao zikhale zizindikiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani anu anabangula pa malo pamene Inu munkakumana nafe; anayimika mbendera zawo monga zizindikiro zachigonjetso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Otsutsana ndi Inu abangula pakati pa msonkhano wanu; Aika mbendera zao zikhale zizindikilo.