Psalms 74:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyumba yanu adaitentha, malo amene Inu mumakhalako adaŵaipitsa poŵagwetsera pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatentha malo anu opatulika; anaipsa ndi kugwetsa pansi mokhalamo dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anatentha malo anu opatulika mpaka kuwagwetsa pansi; anadetsa malo okhalamo dzina lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatentha malo anu opatulika; Anaipsa ndi kugwetsa pansi mokhalamo dzina lanu.