Psalms 75:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene dziko lapansi likugwedezeka pamodzi ndi zonse zokhalamo, ndine amene ndimachirikiza mizati yake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo; ndinachirika mizati yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene dziko lapansi ndi anthu ake onse anjenjemera, ndine amene ndimagwiriziza mizati yake molimba. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo; Ndinacirika mizati yace.