Psalms 75:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimauza anthu odzitama kuti, “Musadzitame,” ndiponso anthu oipa kuti, “Musadzitukumule chifukwa cha mphamvu zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinati kwa odzitamandira, musamachita zodzitamandira; ndi kwa oipa, Musamakweza nyanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa odzitama ndikuti, ‘Musadzitamenso,’ ndipo kwa oyipa, ‘Musatukulenso nyanga zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinati kwa odzitamandira, Musamacita zodzitamandira; Ndi kwa oipa, Musamakweza nyanga;