Psalms 75:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndi Mulungu yekha amene amagamula milandu, amatsitsa wina, nakweza wina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mulungu ndiye woweruza; achepsa wina, nakuza wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndi Mulungu amene amaweruza: Iyeyo amatsitsa wina, nakwezanso wina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Mulungu ndiye woweruza; Acepsa wina, nakuza wina.