Psalms 75:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine sindidzaleka kukondwera, ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wa Yakobe mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndidzalalikira kosalekeza, ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wa Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena za ine, ndidzalengeza izi kwamuyaya; ndidzayimba matamando kwa Mulungu wa Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndidzalalikira kosalekeza, Ndidzayimbira zomlemekeza Mulungu wa Yakobo.