Psalms 76:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndi wodziŵika m'dziko la Yuda, dzina lake ndi lolemekezeka mu Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Neginoto. Salimo la Asafu. Nyimbo. Mulungu adziwika mwa Yuda, dzina lake limveka mwa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Pa zoyimbira za zingwe. Salimo la Asafu. Mulungu amadziwika mu Yuda; dzina lake ndi lotchuka mu Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu adziwika mwa Yuda: Dzina lace limveka mwa Israyeli.