Psalms 76:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, mkwiyo wa anthu umabweretsa ulemu kwa Inu, opulumuka ku mkwiyowo mumaŵasunga pafupi ndi Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indedi, kuzaza kwake kwa munthu kudzakulemekezani; chotsalira cha kuzazaku mudzachiletsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zoonadi, ukali wanu pa anthu umakubweretserani matamando ndipo opulumuka ku ukali wanu mumawasunga pafupi nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indedi, kuzaza kwace kwa munthu kudzakulemekezani; Cotsalira ca kuzazaku mudzaciletsa.