Psalms 76:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiye amene amathetsa mphamvu akalonga ndipo amaopsa mafumu a pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye adzadula mzimu wa akulu; akhala woopsa kwa mafumu a pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amaswa mzimu wa olamulira; amaopedwa ndi mafumu a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye adzadula mzimu wa akulu; Akhala woopsa kwa mafumu a pa dziko lapansi.