Psalms 76:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mukuwonetsa ulemerero ndi mphamvu kupambana mapiri a zofunkha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli achifwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolemekezeka ndinu, wamphamvu kuposa mapiri amene ali ndi nyama zambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli acifwamba.