Psalms 76:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudalanda zofunkha za anthu olimba mtima, mudaŵagonetsa tulo tofa nato, ankhondo onse sankatha kuchita kanthu ndi manja ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Olimba mtima chifunkhidwa chuma chao, agona tulo tao; amuna onse amphamvu asowa manja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu owuma mtima amagona atalandidwa chuma, Iwowo amagona tulo tawo totsiriza; palibe mmodzi wamphamvu amene angatukule manja ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Olimba mtima cifunkhidwa cuma cao, agona tulo tao; Amuna onse amphamvu asowa manja ao.