Psalms 76:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mudaŵaopsa, Inu Mulungu wa Yakobe, onse okwera pa akavalo ndi akavalo ao omwe adagwa nangoti kakasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa kudzudzula kwanu, Mulungu wa Yakobo, galeta ndi kavalo yemwe anagwa m'tulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa kudzudzula kwanu, Inu Mulungu wa Yakobo, kavalo pamodzi ndi galeta zimakhala chete zitagona pansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa kudzudzula kwanu, Mulungu wa Yakobo, Gareta ndi kavalo yemwe anagwa m'tulo.