Psalms 76:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chiweruzo chanu mudachilengeza kumwamba, anthu a pa dziko lapansi adaopa nakhala chete,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudamveketsa chiweruzo chochokera Kumwamba; dziko lapansi linachita mantha, nilinakhala chete,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera kumwamba Inu munalengeza chiweruzo, ndipo dziko linaopa ndi kukhala chete,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudamveketsa ciweruzo cocokera Kumwamba; Dziko lapansi linacita mantha, nilinakhala cete,