Psalms 76:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene Inu Mulungu mudaimirira kuti muweruze anthu, ndi kupulumutsa opsinjidwa onse a pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuuka Mulungu kuti aweruze, kuti apulumutse ofatsa onse a pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamene Inu Mulungu munadzuka kuti muweruze, kupulumutsa onse osautsidwa mʼdziko. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuuka Mulungu kuti aweruze, Kuti apulumutse ofatsa onse a pa dziko lapansi.