Psalms 77:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikulira mopemba kwa Mulungu, ndi mau okweza ndikufuula kwa Mulungu kuti andimve.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Yedutuni; Salimo la Asafu. Ndidzafuulira kwa Mulungu ndi mau anga; kwa Mulungu ndi mau anga, ndipo adzanditcherezera khutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Potsata mayimbidwe a Yedutuni. Salimo la Asafu. Ndinafuwulira Mulungu kupempha thandizo; ndinafuwula mokweza kwa Mulungu kuti anditcherere khutu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzapfuulira kwa Mulungu ndi mau anga; Kwa Mulungu ndi mau anga, ndipo adzandicherezera khutu.