Psalms 77:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chondiŵaŵa ndi chakuti, Mulungu Wopambanazonse wasintha mchitidwe wake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinati, Chindilaka ichi; koma ndikumbukira zaka za dzanja lamanja la Wam'mwambamwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndinaganiza, “Pa izi ine ndidzapemphanso: zaka za dzanja lamanja la Wammwambamwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinati, Cindilaka ici; Koma ndikumbukila zaka za dzanja lamanja la Wam'mwambamwamba.