Psalms 77:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Njira zanu, Inu Mulungu, nzoyera. Kodi alipo mulungu winanso wamkulu ngati Mulungu wathu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu, m'malo opatulika muli njira yanu; Mulungu wamkulu ndani monga Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Njira zanu Mulungu ndi zoyera. Kodi ndi mulungu uti ali wamkulu kuposa Mulungu wathu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu, m'malo opatulika muli njira yanu; Mulungu wamkuru ndani monga Mulungu?