Psalms 77:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu ndinu Mulungu amene mumachita zodabwitsa, amene mwaonetsa mphamvu zanu pakati pa mitundu ya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu ndinu Mulungu wakuchita chodabwitsa; munazindikiritsa mphamvu yanu mwa mitundu ya anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu ndinu Mulungu wochita zodabwitsa; Mumaonetsera mphamvu yanu pakati pa mitundu ya anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu ndinu Mulungu wakucita codabwiza; Munazindikiritsa mphamvu yanu mwa mitundu ya anthu.