Psalms 77:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudaombola anthu anu ndi mkono wanu wamphamvu, ndiye kuti ana a Yakobe ndi Yosefe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munaombola anthu anu ndi mkono wanu, ndiwo ana a Yakobo, ndi a Yosefe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi dzanja lanu lamphamvu munawombola anthu anu, zidzukulu za Yakobo ndi Yosefe. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munaombola anthu anu ndi mkonowanu, Ndiwo ana a Yakobo, ndi a Yosefe.