Psalms 77:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene madzi adakuwonani, Inu Mulungu, pamene madzi adakuwonani, adachita mantha, inde, nyanja yakuya idanjenjemera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Madziwo anakuonani Mulungu; anakuonani madziwo; anachita mantha, zozama zomwe zinanjenjemera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madzi anakuonani Mulungu, madzi anakuonani ndipo anachita mantha; nyanja yozama inakomoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Madziwo anakuonani Mulungu; Anakuonani madziwo; anacita mantha: Zozama zomwe zinanjenjemera,