Psalms 77:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitambo idachucha madzi, mumlengalenga mudachita bingu. Zing'aning'ani mbali ndi mbali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Makongwa anatsanula madzi; thambo lidamvetsa liu lake; mivi yanu yomwe inatulukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitambo inakhuthula madzi ake pansi, mu mlengalenga munamveka mabingu; mivi yanu inawuluka uku ndi uku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Makongwa anatsanula madzi; Thambo lidamvetsa liu lace; Mibvi yanu yomwe inaturukira.