Psalms 77:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phokoso la bingu lanu lidamveka konsekonse, mphezi zanu zidaŵalitsa dziko lonse, dziko lapansi lidanjenjemera ndi kugwedezeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Liu la bingu lanu linatengezanatengezana; mphezi zinaunikira ponse pali anthu; dziko lapansi linanjenjemera ndi kugwedezeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bingu lanu linamveka mʼmphepo ya kamvuluvulu, mphenzi yanu inawalitsa dziko lonse; dziko lapansi linanjenjemera ndi kugwedezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Liu la bingu lanu linatengezanatengezana; Mphezi zinaunikira ponse pali anthu; Dziko lapansi linanjenjemera ndi kugwedezeka.