Psalms 77:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudadzera pa nyanja, njira yanu idadzera pa madzi akuya, komabe mapazi anu sadaoneke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njira yanu inali m'nyanja, koyenda Inu nku madzi aakulu, ndipo mapazi anu sanadziwike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Njira yanu inadutsa pa nyanja, njira yanu inadutsa pa madzi amphamvu, ngakhale zidindo za mapazi anu sizinaoneke.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njira yanu inali m'nyanja, Koyenda Inu nku madzi akulu, Ndipo mapazi anu sanadziwika.