Psalms 77:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lamavuto ndimafunafuna Ambuye. Usiku wonse ndimakweza manja anga ndi kupemphera kosalekeza. Mtima wanga umakana kuusangalatsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku la nsautso yanga ndinafuna Ambuye. Dzanja langa linatambalika usiku, losaleka; mtima wanga unakana kutonthozedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinali pa masautso ndinafunafuna Ambuye; usiku ndinatambasula manja mosalekeza ndipo moyo wanga unakana kutonthozedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku la nsautso yanga ndinafuna Ambuye: Dzanja langa linatambalika usiku, losaleka; Mtima wanga unakanakutonthozedwa.