Psalms 77:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudatsogolera anthu anu ngati nkhosa kudzera mwa Mose ndi Aroni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munatsogolera anthu anu ngati gulu la nkhosa, ndi dzanja la Mose ndi Aroni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munatsogolera anthu anu ngati gulu la nkhosa mwa dzanja la Mose ndi Aaroni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munatsogolera anthu anu ngati gulu la nkhosa, Ndi dzanja la Mose ndi Aroni,