Psalms 77:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumagwira zikope zanga kuti ndisagone tulo. Ndikuvutika kwambiri kotero kuti sindingathe kulankhula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundikhalitsa maso; ndigwidwa mtima wosanena kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munagwira zikope zanga kuti ndisagone ndipo ndinavutika kwambiri kuti ndiyankhule.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundikhalitsa maso; Ndigwidwa mtima wosanena kanthu.