Psalms 77:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimalingalira za masiku akale, ndimakumbukira zaka zamakedzana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinaganizira masiku akale, zaka zakalekale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinaganizira za masiku akale, zaka zamakedzana;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinaganizira masiku akale, zaka zakalekale.