Psalms 77:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimasinkhasinkha mumtima mwanga usiku. Ndimadzifunsa ndi kufufuzafufuza mumtima mwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikumbukira nyimbo yanga usiku; ndilingalira mumtima mwanga; mzimu wanga unasanthula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinakumbukira nyimbo zanga usiku. Mtima wanga unasinkhasinkha ndipo mzimu wanga unafunsa kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikumbukila Nyimbo yanga, usiku; Ndilingalira mumtima mwanga; Mzimu wanga unasanthula.