Psalms 77:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Mulungu waiŵala kukoma mtima kwake kuja? Kodi wakwiya ndi kuleka chifundo chake chija?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Mulungu waiwala kuchita chifundo? Watsekereza kodi nsoni zokoma zake mumkwiyo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Mulungu wayiwala kukhala wokoma mtima? Kodi mu mkwiyo wake waleka chifundo chake?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Mulungu waiwala kucita cifundo? Watsekereza kodi nsoni zokoma zace mumkwiyo?