Psalms 78:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adachita zodabwitsa zake, makolo ao akuwona, m'dziko la Ejipito, ku dera la Zowani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anachita chodabwitsa pamaso pa makolo ao, m'dziko la Ejipito kuchidikha cha Zowani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo anachita zodabwitsa makolo athu akuona, mʼdziko la Igupto, mʼchigawo cha Zowani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anacita codabwiza pamaso pa makolo ao, M'dziko la Aigupto ku cidikha ca Zoanu.