Psalms 78:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adagaŵa nyanja pakati, kuti iwo apitepo, ndipo adaimiritsa madzi ngati makoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anagawa nyanja nawapititsapo; naimitsa madziwo ngati khoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anagawa nyanja pakati ndi kudutsitsapo iwowo, Iye anachititsa madzi kuyima chilili ngati khoma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anagawa nyanja nawapititsapo; Naimitsa madziwo ngati khoma.