Psalms 78:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adang'amba matanthwe am'chipululu, naŵapatsa madzi ochuluka ngati amumtsinje, kuti amwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anang'alula thanthwe m'chipululu, ndipo anawamwetsa kochuluka monga m'madzi ozama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anangʼamba miyala mʼchipululu ndi kuwapatsa madzi ochuluka ngati a mʼnyanja zambiri;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anang'alula thanthwe m'cipululu, Ndipo anawamwetsa kocuruka monga m'madzi ozama.