Psalms 78:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adayesa Mulungu m'mitima mwao, pomuumiriza kuti aŵapatse chakudya chimene ankakhumba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayesa Mulungu mumtima mwao ndi kupempha chakudya monga mwa kulakalaka kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ananyoza Mulungu mwadala pomuwumiriza kuti awapatse chakudya chimene anachilakalaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayesa Mulungu mumtimamwao Ndi kupempha cakudya monga mwa kulakalaka kwao.