Psalms 78:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja adamenya thanthwe, kotero kuti madzi adatumphuka, ndipo mitsinje idadzaza. Kodi angathenso kutipatsa ife anthu ake buledi kapena kutipezera nyama?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, anapanda thanthwe, ndi madzi anayendako ndi mitsinje inasefuka; kodi adzakhozanso kupatsa mkate? Kodi adzafunira anthu ake nyama?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye atamenya thanthwe madzi anatuluka, ndipo mitsinje inadzaza ndi madzi. Koma iye angatipatsenso ife chakudya? Kodi angapereke nyama kwa anthu akewa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, anapanda thanthwe, ndi madzi anayendako Ndi mitsinje inasefuka; Kodi adzakhozanso kupatsa mkate? Kodi adzafunira anthu ace nyama?