Psalms 78:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Chauta atamva zimenezi, adapsa mtima kwambiri, adayatsira moto Yakobe, napambana kukwiyira Israeleyo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Yehova anamva, nakwiya; ndipo anayatsa moto pa Yakobo, ndiponso mkwiyo unakwera pa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova atawamva anakwiya kwambiri; moto wake unayaka kutsutsana ndi Yakobo, ndipo mkwiyo wake unauka kutsutsana ndi Israeli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Yehova anamva, nakwiya; Ndipo anayatsa moto pa Yakobo, Ndiponso mkwiyo unakwera pa Israyeli;