Psalms 78:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Iye adalamula mitambo yamumlengalenga, natsekula zitseko zakumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma analamulira mitambo ili m'mwamba, natsegula m'makomo a kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe Iye anapereka lamulo kwa mitambo mmwamba ndi kutsekula makomo a mayiko akumwamba;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma analamulira mitambo iri m'mwamba, Natsegula m'makomo a kumwamba.