Psalms 78:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poŵagwetsera mana kuti adye, adaŵapatsa tirigu wakumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawavumbitsira mana, adye, nawapatsa tirigu wa kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anagwetsa mana kuti anthu adye, anawapatsa tirigu wakumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawabvumbitsira mana, adye, Nawapatsa tirigu wa kumwamba.