Psalms 78:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu adadya buledi wa angelo, ndipo Mulungu adaŵatumizira chakudya chochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yense anadya mkate wa angelo, anawatumizira chakudya chofikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu anadya buledi wa angelo, Iye anawatumizira chakudya chonse chimene akanatha kudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yense anadya mkate wa omveka: Anawatumizira cakudya cofikira,