Psalms 78:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵagwetsera nyama yochuluka ngati fumbi, mbalame zochuluka ngati mchenga wakunyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawavumbitsira nyama ngati fumbi, ndi mbalame zouluka ngati mchenga wa kunyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawagwetsera nyama ngati fumbi, mbalame zowuluka ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawabvumbitsira nyama ngati pfumbi, Ndi mbalame zouluka ngati mcenga wa kunyanja: