Psalms 78:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adadya nakhuta kwambiri, popeza kuti adaŵapatsa zakudya zimene ankakhumba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero anadya nakhuta kwambiri; ndipo anawapatsa chokhumba iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anadya mpaka anatsala nazo zochuluka pakuti Iye anawapatsa zimene anazilakalaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero anadya nakhuta kwambiri; Ndipo anawapatsa cokhumba iwo.