Psalms 78:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma nkhuli yao isanathe, asanameze nkumeza komwe chakudya chaocho,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asanathe nacho chokhumba chao, chakudya chao chili m'kamwa mwao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iwowo anasiya kudya chakudya anachilakalakacho, chakudya chili mʼkamwa mwawobe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asanathe naco cokhumba cao, Cakudya cao ciri m'kamwa mwao,