Psalms 78:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mkwiyo wa Mulungu udaŵayakira, ndipo adapha amphamvu onse pakati pao, adapha anyamata abwinoabwino onse a mu Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo mkwiyo wa Mulungu unawaukira, ndipo anapha mwa onenepa ao, nagwetsa osankhika a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mkwiyo wa Mulungu unawayakira; Iye anapha amphamvu onse pakati pawo, kugwetsa anyamata abwino kwambiri mu Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mkwiyo wa Mulungu unawaukira, Ndipo anapha mwa onenepa ao, Nagwetsa osankhika a Israyeli.