Psalms 78:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Mulungu adadula masiku ao kuti azimirire ngati mpweya, adadula zaka zao kuti zithere m'zoopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero anathera masiku ao ndi zopanda pake, ndi zaka zao mwa mantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Mulungu anachepetsa masiku awo kuti azimirire ngati mpweya. Iye anachepetsa zaka zawo kuti zithere mʼmasautso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero anathera masiku ao ndi zopanda pace, Ndi zaka zao mwa mantha.