Psalms 78:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ankapha ena, otsalira ankayamba kumufunafuna. Ankalapa namafunafuna Mulungu ndi mtima wao wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene anawapha ndipo anamfuna Iye; nabwerera, nafunitsitsa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu atawapha, iwo amamufunafuna Iyeyo; iwo ankatembenukiranso kwa Iye mwachangu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene anawapha ndipo anamfuna Iye; Nabwerera, nafunitsitsa Mulungu,