Psalms 78:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe pakuti Mulungu ngwachifundo, adaŵakhululukira machimo ao, ndipo sadaŵaononge. Kaŵirikaŵiri ankadziletsa kukwiya, sadalole kuti mkwiyo wake wonse uyake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye pokhala ngwa chifundo, anakhululukira choipa, osawaononga; nabweza mkwiyo wake kawirikawiri, sanautse ukali wake wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe Iye anali wachifundo; anakhululukira mphulupulu zawo ndipo sanawawononge. Nthawi ndi nthawi Iye anabweza mkwiyo wake ndipo sanawutse ukali wake wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Iye pokhala ngwa cifundo, Anakhululukira coipa, osawaononga; Nabweza mkwiyo wace kawiri kawiri, Sanautsa ukali wace wonse.